Luka 13:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

onani nyumba yanu isiyidwa kwa inu yabwinja; ndipo ndinena kwa inu kuti, Simudzandiona Ine, kufikira mudzati, Wolemekezeka iye amene akudza m'dzina la Ambuye.

Luka 13

Luka 13:28-35