Luka 13:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati kwa iwo, Pitani kauzeni nkhandweyo, Taonani, nditurutsa ziwanda, nditsiriza maciritso lero ndi mawa, ndipo mkuca nditsirizidwa.

Luka 13

Luka 13:28-35