Luka 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anayankha nati kwa iwo, Kodi muyesa kuti Agalileya aja anali anthu akucimwa koposa Agalileya onse, cifukwa anamva zowawa izi?

Luka 13

Luka 13:1-5