Luka 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Iye anatero, onse aja akutsutsana naye ananyazitsidwa; ndipo anthu onse a m'khamu anakondwera ndi zinthu zonse za ulemererozo zinacitidwa ndi iye.

Luka 13

Luka 13:12-26