Luka 13:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkazi anali nao mzimu wakumdwalitsa zaka khumi ndi zisanu ndi zitatu; nakhala wopeteka, ndimo analibe mphamvu konse yakuweramuka.

Luka 13

Luka 13:6-14