Luka 12:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma 2 kapolo uyo akanena mumtima mwace, Mbuye wanga azengereza kudza; ndimo akayamba kupanda anyamata ndi adzakazi ndi kudya ndi kumwa, ndi kuledzera;

Luka 12

Luka 12:39-51