Luka 12:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lingirirani makungubwi, kuti samafesai, kapena kutemai; alibe nyumba yosungiramo, kapena nkhokwe; ndipo Mulungu awadyetsa: nanga inu simuziposa mbalame kwambiri!

Luka 12

Luka 12:22-32