Luka 12:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mulungu anati kwa iye, Wopusa iwe, usiku womwe uno udzafunidwa moyo wako; ndipo zinthu zimene unazikonza zidzakhala za yani?

Luka 12

Luka 12:18-21