Luka 11:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene iye anaturuka m'menemo, alembi ndi Afarisi anayamba kumuumiriza iye kolimba, ndi kumtompha iye ndi zinthu zambiri;

Luka 11

Luka 11:45-54