Luka 11:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco muli mboni, ndipo mubvomera nchito za makolo anu; cifukwa iwotu anawapha, koma inu muwamangira iwo zapamanda.

Luka 11

Luka 11:39-54