Luka 11:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ambuye anati kwa iye, Tsopano inu Afarisi muyeretsa kunja kwace kwa cikho ndi mbale, koma m'kati mwanu mudzala zolanda ndi zoipa.

Luka 11

Luka 11:34-41