Luka 11:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo, ngati thupi lako lonse liunikidwa losakhala nalo dera lace lamdima, lidzakhala lounikidwa monsemo, ngati pamene nyali ndi kuwala kwace ikuunikira iwe.

Luka 11

Luka 11:33-37