Luka 11:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe munthu, atayatsa nyali, aiika m'cipinda capansi, kapena pansi pa muyeso, koma pa coikapo cace, kuti iwo akulowamo aone kuunika.

Luka 11

Luka 11:31-36