Luka 11:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo, upita nutenga mizimu yina isanu ndi iwiri yoipa yoposa ndi uwu mwini; ndipo ilowa nikhalira komweko; ndipo makhalidwe otsiriza a munthu uyu aipa koposa oyambawo.

Luka 11

Luka 11:23-35