Luka 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, ngati inu, okhala oipa, mudziwa kupatsa ana anu mphatso zabwino, koposa kotani nanga Atate wanu wa Kumwamba adzapatsa Mzimu Woyera kwa iwo akumpempha iye?

Luka 11

Luka 11:9-18