Luka 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'nyumba momwemo khalani, ndi kudya ndi kumwa za kwao; pakuti wanchito ayenera mphotho yace; musacokacoka m'nyumba.

Luka 10

Luka 10:1-8