Luka 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndinena ndi inu kuti 1 aneneri ndi mafumu ambiri anafuna kuona zimene inu muziona, koma sanaziona; ndi kumva zimene mukumva, koma sanazimva.

Luka 10

Luka 10:22-25