Luka 1:61-63 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

61. Ndipo iwo anati kwa iye, Palibe wina wa abale ako amene achedwa dzina ili.

62. Ndipo anakodola atate wace, afuna amuche dzina liti?

63. Ndipo iye anafunsa colemberapo, nalemba, kuti, Dzina lace ndi Yohane. Ndipo anazizwa onse.

Luka 1