Luka 1:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene Elisabeti anamva kulankhula kwace kwa Mariya, mwana wosabadwayo anatsalima m'mimba mwace; ndipo Elisabeti anadzazidwa ndi Mzimu Woyera;

Luka 1

Luka 1:40-44