Luka 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iye adzakhala wamkuru pamaso pa Ambuye, ndipo sadzamwa konse vinyo kapena, kacasu; nadzadzazidwa ndi Mzimu Woyera, kuyambira asanabadwe.

Luka 1

Luka 1:9-21