Luka 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mngelo anati kwa iye, Usaope Zakariya, cifukwa kuti lamveka pemphero lako, ndipo mkazi wako adzakubalira mwana wamwamuna, ndipo udzamucha dzina lace Yohane.

Luka 1

Luka 1:8-17