Levitiko 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ndi Aroni analowa ku cihema cokomanako, naturuka, nadalitsa anthu; ndipo ulemero wa Yehova unaonekera kwa anthu onse.

Levitiko 9

Levitiko 9:22-24