Levitiko 8:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga mafutawo ndi mcira wamafuta, ndi mafuta onse a pamatumbo, ndi cokuta ca mphafa, ndi imso ziwiri, ndi mafuta ace, ndi mwendo wathako wa ku dzanja lamanja;

Levitiko 8

Levitiko 8:19-34