Levitiko 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwera nayo nkhosa yamphongo yinayo, ndiyo mphongo ya kudzaza manja; ndipo Aroni ndi ana ace amuna anaika manja ao pa mutu wa mphongoyo.

Levitiko 8

Levitiko 8:14-26