Levitiko 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anatenga ana a Aroni, nawabveka maraya a m'kati, nawamanga m'cuuno ndi mipango, nawamanga akapa; monga Yehova adauza Mose.

Levitiko 8

Levitiko 8:8-21