Levitiko 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anawazako pa guwa la nsembe kasanu ndi kawiri, nadzoza guwa la nsembe, ndi zipangizo zace zonse, ndi mkhate ndi tsinde lace, kuzipatula.

Levitiko 8

Levitiko 8:3-19