Levitiko 7:26-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Ndipo musamadya mwazi uti wonse, kapena wa mbalame, kapena wa nyama, m'nyumba zanu zonse,

27. Ali yense akadya mwazi uti wonse, munthuyo asadzidwe kwa anthu a mtundu wace.

28. Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,

Levitiko 7