Levitiko 6:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mota wa pa guwa la nsembe uyakebe pamenepo, wosazima; wansembe ayatsepo nkhuni m'mawa ndi m'mawa; nakonzepo nsembe yopsereza, natenthepo mafuta a nsembe zoyamika.

Levitiko 6

Levitiko 6:11-16