Levitiko 5:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nawazeko mwazi wa nsembe yaucimo pa mbali ya guwa la nsembe; ndi mwazi wotsalira aukamulire patsinde pa guwa la nsembe; ndiyo nsembe yaucimo.

Levitiko 5

Levitiko 5:2-13