Levitiko 4:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe atengeko mwazi ndi cala cace, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wace wonse patsinde pa guwa la nsembe.

Levitiko 4

Levitiko 4:28-35