Levitiko 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akalakwa wansembe wodzozedwa ndi kuparamulira anthu; pamenepo azibwera nayo kwa Yehova ng'ombe yamphongo, yopanda cirema, cifukwa ca kucimwa kwace adakucita, ikhale nsembe yaucimo.

Levitiko 4

Levitiko 4:1-10