Levitiko 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo copereka cace cikakhala nkhosa kapena mbuzi, kuti ikhale nsembe yoyamika ya kwa Yehova; ingakhale yaimuna kapena yaikazi, azibwera nayo yopanda cirema;

Levitiko 3

Levitiko 3:5-12