Levitiko 27:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akakhala munthu wa zaka makumi asanu ndi limodzi ndi mphambu, akakhala wamwamuna, umuyesere wa masekeli khumi ndi asanu, akakhala wamkazi wa masekeli khumi.

Levitiko 27

Levitiko 27:3-14