Levitiko 27:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akaupatula munda wace citapita caka coliza lipenga, wansembe azimwerengera ndalama monga mwa zaka zotsalira kufikira caka coliza lipenga, nazicepsako pa kuyesa kwako.

Levitiko 27

Levitiko 27:11-28