Levitiko 26:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa ndi malemba ndi maweruzo ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Israyeli m'phiri la Sinai, ndi dzanja la Mose.

Levitiko 26

Levitiko 26:44-46