Levitiko 26:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakhumudwitsana monga pothawa lupanga, wopanda wakuwalondola; ndipo mudzakhala opanda mphamvu yakuima pamaso pa adani anu.

Levitiko 26

Levitiko 26:28-44