Levitiko 26:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo dzikoli lidzakondwera nao masabata ace, masiku onse a kupasuka kwace, pokhala inu m'dziko la adani anu; pamenepo dziko lidzapumula, ndi kukondwera nao masabata ace.

Levitiko 26

Levitiko 26:26-42