Levitiko 26:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inenso ndidzayenda motsutsana ndi inu; ndipo ndidzakukanthani Inedi kasanu ndi kawiri cifukwa ca zoipa zanu.

Levitiko 26

Levitiko 26:15-32