Levitiko 25:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muwayese colowa ca ana anu akudza m'mbuyo, akhale ao ao; muwayese akapolo kosatha; koma za abale anu, ana a Israyeli, musamalamulirana mozunza.

Levitiko 25

Levitiko 25:39-52