Levitiko 25:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto, kukupatsani dziko la Kanani, kuti ndikhale Mulungu wanu.

Levitiko 25

Levitiko 25:32-42