Levitiko 23:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku asanu ndi limodzi azigwira nchito; koma lacisanu ndi ciwiri ndilo Sabata lakupumula, msonkhano wopatulika; musamagwira nchito konse; ndilo sabata la Yehova m'nyumba zanu zonse.

Levitiko 23

Levitiko 23:1-13