Levitiko 23:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamadya mkate, kapena tirigu wokazinga, kapena ngala zaziwisi, kufikira tsiku lomweli, kufikira mutadza naco copereka ca Mulungu wanu; ndilo lemba losatha mwa mibadwo yanu m'nyumba zanu zonse.

Levitiko 23

Levitiko 23:13-23