Levitiko 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu ali yense wa mbeu za Aroni wokhala ndi khate, kapena kukha, asadyeko zinthu zopatulika, kufikira atayera. Ndipo ali yense wokhudza cinthu codetsedwa ndi wakufa, kapena mwamuna wogona uipa;

Levitiko 22

Levitiko 22:1-8