Levitiko 22:30-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Idyedwe tsiku lomwelo; musamasiyako kufikira m'mawa; Ine ndine Yehova.

31. Potero muwasunge malamulo anga, ndi kuwacita; Ine ndine Yehova.

32. Musamaipsa dzina langa loyera; koma ndikhale woyera pakati pa ana a Israyeli; Ine ndine Yehova wakukupatulani,

33. amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto, kuti ndikhale Mulungu wanu; Ine ndine Yehova.

Levitiko 22