Levitiko 20:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Unenenso kwa ana a Israyeli ndi kuti, Ali yense wa ana a Israyeli, kapena wa alendo akukhala m'Israyeli, amene apereka mbeu zace kwa Moleke, azimupha ndithu; anthu a m'dziko amponye miyala.

Levitiko 20

Levitiko 20:1-5