Levitiko 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembeyo atengeko cikumbutso pa nsembe yaufa, nacitenthe pa guwa la nsembe; ndico nsembe yamoto ya pfungo lokoma la kwa Yehova.

Levitiko 2

Levitiko 2:2-10