Levitiko 2:15-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Ndipo uthirepo mafuta, ndi kuikapo libona; ndiyo nsembe yaufa.

16. Ndipo wansembe atenthe cikumbutso cace, atatapa pa tirigu wace wokonola, ndi pa mafuta ace, ndi kutenga libano lace lonse; ndiyo nsembe yamoto ya kwa Yehova.

Levitiko 2