Levitiko 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akagona ndi mkazi, ndiye mdzakazi, wopalidwa ubwenzi ndi mwamuna, wosamuombola kapena wosapatsidwa ufulu, akwapulidwe; asawaphe, popeza si mfulu mkaziyo.

Levitiko 19

Levitiko 19:12-29