Levitiko 19:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usamasautsa mnansi wako, kapena kulanda zace; mphotho yace ya wolipidwa isakhale ndi iwe kufikira m'mawa.

Levitiko 19

Levitiko 19:8-22