Levitiko 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usamakunkha khunkha la m'munda wako wamphesa, usamazitola zidagwazi za m'munda wako wamphesa; uzisiyire wosauka ndi mlendo; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Levitiko 19

Levitiko 19:8-13